Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 poika moyo wake pangozi+ pamene anakumenyerani nkhondo+ kuti akulanditseni m’manja mwa Amidiyani?+

  • Oweruza 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nditaona kuti inu simukubwera kudzandipulumutsa, ndinalolera kufa,* moti ndinapita kukamenyana ndi ana a Amoni,+ ndipo Yehova anawapereka m’manja mwanga.+ Tsopano n’chifukwa chiyani lero mwabwera kudzandiukira kuti mumenyane nane?”

  • 1 Samueli 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno mkazi uja anapita pamene panali Sauli ndipo anaona kuti wathedwa nzeru kwambiri. Choncho anamuuza kuti: “Ineyo mtumiki wanu ndamvera mawu anu ndipo ndaika moyo wanga pangozi*+ pomvera mawu amene mwandiuza.

  • Salimo 119:109
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 109 Moyo wanga uli pangozi nthawi zonse,*+

      Koma sindinaiwale chilamulo chanu.+

  • Machitidwe 20:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Komabe, moyo wanga sindikuuona ngati wofunika kapena wamtengo wapatali kwa ine ayi.+ Chimene ndikungofuna n’chakuti ndimalize kuthamanga mpikisano umenewu,+ komanso kuti ndimalize utumiki+ umene ndinalandira+ kwa Ambuye Yesu basi. Ndikungofuna kuchitira umboni mokwanira za uthenga wabwino wa kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+

  • Afilipi 2:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 pakuti chifukwa cha ntchito ya Ambuye, anatsala pang’ono kufa.+ Anaika moyo wake pachiswe, kuti adzanditumikire m’malo mwa inu,+ popeza simuli kuno.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena