2 Timoteyo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndamenya nkhondo yabwino.+ Ndathamanga panjirayo mpaka pa mapeto pake.+ Ndasunga chikhulupiriro.+