1 Akorinto 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero, sikuti ndikungothamanga+ osadziwa kumene ndikulowera. Mmene ndikuponyera nkhonya zanga, sikuti ndikungomenya mphepo ayi,+ 1 Timoteyo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.
26 Motero, sikuti ndikungothamanga+ osadziwa kumene ndikulowera. Mmene ndikuponyera nkhonya zanga, sikuti ndikungomenya mphepo ayi,+
12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.