Agalatiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo,+ ndine mtumwi,+ osati wochokera kwa anthu kapena woikidwa kudzera mwa munthu, koma mwa Yesu Khristu+ ndi mwa Mulungu Atate+ amene anamuukitsa kwa akufa.+
1 Ine Paulo,+ ndine mtumwi,+ osati wochokera kwa anthu kapena woikidwa kudzera mwa munthu, koma mwa Yesu Khristu+ ndi mwa Mulungu Atate+ amene anamuukitsa kwa akufa.+