Machitidwe 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno iye anati, ‘Mulungu wa makolo athu+ wakusankha+ kuti udziwe chifuniro chake, ndi kuti uone+ Wolungamayo+ ndi kumva mawu a pakamwa pake.+
14 Ndiyeno iye anati, ‘Mulungu wa makolo athu+ wakusankha+ kuti udziwe chifuniro chake, ndi kuti uone+ Wolungamayo+ ndi kumva mawu a pakamwa pake.+