1 Akorinto 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye n’zimene inenso ndinakupatsirani, zakuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anali kukaperekedwa anatenga mkate. Agalatiya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uthengawu sindinaulandire kwa munthu, ndipo sindinachite kuuphunzira mwanjira ina, koma Yesu Khristu ndiye amene anandiululira uthenga umenewu.+
23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye n’zimene inenso ndinakupatsirani, zakuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anali kukaperekedwa anatenga mkate.
12 Uthengawu sindinaulandire kwa munthu, ndipo sindinachite kuuphunzira mwanjira ina, koma Yesu Khristu ndiye amene anandiululira uthenga umenewu.+