Aroma 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake. Tito 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, kapolo+ wa Mulungu ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndili ndi chikhulupiriro chogwirizana ndi cha anthu osankhidwa+ ndi Mulungu. Komanso ndine wodziwa molondola+ choonadi+ chokhudza kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+
5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake.
1 Ine Paulo, kapolo+ wa Mulungu ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndili ndi chikhulupiriro chogwirizana ndi cha anthu osankhidwa+ ndi Mulungu. Komanso ndine wodziwa molondola+ choonadi+ chokhudza kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+