2 Timoteyo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa chifukwa chimenechi, ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ kuti iwonso alandire chipulumutso chimene chimabwera chifukwa chokhala ogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso alandire ulemerero wosatha.+
10 Pa chifukwa chimenechi, ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ kuti iwonso alandire chipulumutso chimene chimabwera chifukwa chokhala ogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso alandire ulemerero wosatha.+