Mateyu 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Pakuti oitanidwa ndi ambiri, koma osankhidwa ndi owerengeka.”+ 2 Akorinto 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ngati tili m’masautso, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe ndi kupulumutsidwa.+ Ngati tikutonthozedwa, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe kuti mupirire masautso amene ifenso tikukumana nawo.+ Aefeso 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu. Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+
6 Tsopano ngati tili m’masautso, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe ndi kupulumutsidwa.+ Ngati tikutonthozedwa, cholinga chake ndi choti inuyo mutonthozedwe kuti mupirire masautso amene ifenso tikukumana nawo.+
13 N’chifukwa chake ndikukupemphani kuti musabwerere m’mbuyo poona masautso+ angawa, amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, pakuti akutanthauza ulemerero kwa inu.
24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+