Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+ 2 Timoteyo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa chifukwa chimenechi, ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ kuti iwonso alandire chipulumutso chimene chimabwera chifukwa chokhala ogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso alandire ulemerero wosatha.+
22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+
10 Pa chifukwa chimenechi, ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ kuti iwonso alandire chipulumutso chimene chimabwera chifukwa chokhala ogwirizana ndi Khristu Yesu, ndiponso alandire ulemerero wosatha.+