Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Akolose 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mulungu anaululira anthu a mitundu ina chinsinsi chopatulikachi,+ chimene chili chodzaza ndi ulemerero ndi chuma chauzimu.+ Chinsinsicho n’chakuti Khristu+ ndi wogwirizana ndi inuyo, zimene zikutanthauza kuti muli ndi chiyembekezo chodzalandira ulemerero pamodzi naye.+

  • 2 Atesalonika 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anakuitanani ku chipulumutso chimenechi kudzera mu uthenga wabwino umene tikulengeza,+ kuti mudzapeze ulemerero wa Ambuye wathu Yesu Khristu.+

  • 1 Petulo 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mukavutika kwa kanthawi,+ Mulungu, yemwe amapereka kukoma mtima konse kwakukulu, amenenso anakuitanirani ku ulemerero wake wosatha+ kudzera mu mgwirizano wanu+ ndi Khristu, adzamalizitsa kukuphunzitsani. Adzakulimbitsani+ ndi kukupatsani mphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena