Aroma 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife. 1 Timoteyo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu+ Mpulumutsi wathu,+ ndi Khristu Yesu yemwe ali chiyembekezo chathu,+
18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife.
1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu+ Mpulumutsi wathu,+ ndi Khristu Yesu yemwe ali chiyembekezo chathu,+