Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu. Yuda 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+
3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.
25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+