Aroma 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+ 1 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ndi bwino kuvutika chifukwa chochita zabwino,+ ngati Mulungu walola, kusiyana ndi kuvutika chifukwa chochita zoipa.+ 1 Petulo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.
17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+
17 Pakuti ndi bwino kuvutika chifukwa chochita zabwino,+ ngati Mulungu walola, kusiyana ndi kuvutika chifukwa chochita zoipa.+
16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.