Machitidwe 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Petulo anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese+ mzimu wa Yehova? Taona! Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako m’manda ali pakhomo. Iwenso akunyamula ndi kutuluka nawe.” 1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+
9 Pamenepo Petulo anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese+ mzimu wa Yehova? Taona! Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako m’manda ali pakhomo. Iwenso akunyamula ndi kutuluka nawe.”
15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+