Ekisodo 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose kuti:+ “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana ndi ine? N’chifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+ Salimo 95:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anandisanthula, ndipo anaonanso ntchito zanga.+ Mateyu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Malemba amatinso, ‘Usamuyese Yehova Mulungu wako.’”+ Luka 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Pajatu Malemba amati, ‘Usamuyese, Yehova Mulungu wako.’”+ 1 Akorinto 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+
2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose kuti:+ “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana ndi ine? N’chifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+