Deuteronomo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Musamuyese, Yehova Mulungu wanu,+ mmene munamuyesera pa Masa.*+ Luka 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Pajatu Malemba amati, ‘Usamuyese, Yehova Mulungu wako.’”+ 1 Akorinto 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+