1 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi kupirira kumenyedwa mbama mutachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma ngati mukupirira povutika chifukwa cha kuchita zabwino,+ zimenezo n’zabwino kwa Mulungu.+
20 Kodi kupirira kumenyedwa mbama mutachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma ngati mukupirira povutika chifukwa cha kuchita zabwino,+ zimenezo n’zabwino kwa Mulungu.+