1 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi kupirira pamene mukumenyedwa chifukwa choti mwachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma Mulungu amasangalala mukamapirira mavuto chifukwa choti mukuchita zabwino.+ 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:20 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 59
20 Kodi kupirira pamene mukumenyedwa chifukwa choti mwachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma Mulungu amasangalala mukamapirira mavuto chifukwa choti mukuchita zabwino.+