-
Afilipi 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zidzatero mogwirizana n’kuti ndikudikira mwachidwi,+ ndiponso ndili ndi chiyembekezo+ chakuti sindidzachititsidwa manyazi+ mwa njira iliyonse. Koma kuti mwa ufulu wanga wonse wa kulankhula,+ Khristu alemekezedwe mwa thupi langa tsopano, monga mmene zakhala zikuchitikira m’mbuyo monsemu.+ Kaya ndikhala ndi moyo kapena ndimwalira.+
-
-
Aheberi 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tichite zimenezi pamene tikuyang’anitsitsa Mtumiki Wamkulu+ ndi Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu,+ Yesu. Chifukwa cha chimwemwe chimene anamuikira patsogolo pake,+ anapirira mtengo wozunzikirapo.* Iye sanasamale kuti zochititsa manyazi zimuchitikira, ndipo tsopano wakhala pansi kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu.+
-