1 Akorinto 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu adzakulimbitsani+ mpaka pa mapeto, kuti musakhale ndi chifukwa chokunenezerani+ m’tsiku+ la Ambuye wathu Yesu Khristu.+ Afilipi 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndikutsimikizira kuti iyeyo amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza ndi kuimalizitsa+ m’tsiku+ la Yesu Khristu.
8 Mulungu adzakulimbitsani+ mpaka pa mapeto, kuti musakhale ndi chifukwa chokunenezerani+ m’tsiku+ la Ambuye wathu Yesu Khristu.+
6 Pakuti ndikutsimikizira kuti iyeyo amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza ndi kuimalizitsa+ m’tsiku+ la Yesu Khristu.