Aroma 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti chilengedwe+ chikudikira mwachidwi+ nthawi imene ulemelero wa ana a Mulungu udzaonekere.+