-
Afilipi 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zimenezi nʼzogwirizana ndi zimene ndikudikirira mwachidwi ndiponso chiyembekezo changa chakuti sindidzachititsidwa manyazi mwa njira iliyonse. Koma kuti mwa ufulu wanga wonse wa kulankhula, tsopano Khristu alemekezedwa kudzera mwa ine,* ngati mmene zakhala zikuchitikira mʼmbuyo monsemu. Iye alemekezedwabe kaya ndikhala ndi moyo kapena ndimwalira.+
-