Aroma 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti tikakhala ndi moyo, timakhalira moyo Yehova,*+ ndipo tikafa, timafera Yehova.+ Chotero kaya tikhale ndi moyo kapena tife, ndife a Yehova.+ 1 Petulo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.
8 Pakuti tikakhala ndi moyo, timakhalira moyo Yehova,*+ ndipo tikafa, timafera Yehova.+ Chotero kaya tikhale ndi moyo kapena tife, ndife a Yehova.+
16 Koma ngati akuvutika+ chifukwa chokhala Mkhristu, asachite manyazi,+ koma apitirize kulemekeza Mulungu m’dzina la Khristuyo.