Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+ Agalatiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwa chilamulo, ine ndinafa ku chilamulo,+ moti sindingachitsatirenso, kuti ndikhale wamoyo kwa Mulungu.+ 1 Petulo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
19 Mwa chilamulo, ine ndinafa ku chilamulo,+ moti sindingachitsatirenso, kuti ndikhale wamoyo kwa Mulungu.+
2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+