2 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero chiyembekezo chathu mwa inu sichikugwedera, podziwa kuti mukukumana ndi masautso ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, inunso mudzatonthozedwa ngati ifeyo.+ Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+ 1 Petulo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Okondedwa, musadabwe ndi moto umene ukuyaka pakati panu, ngati kuti mukukumana ndi chinthu chachilendo. Motowo ukuyaka pofuna kukuyesani.+
7 Chotero chiyembekezo chathu mwa inu sichikugwedera, podziwa kuti mukukumana ndi masautso ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, inunso mudzatonthozedwa ngati ifeyo.+
24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+
12 Okondedwa, musadabwe ndi moto umene ukuyaka pakati panu, ngati kuti mukukumana ndi chinthu chachilendo. Motowo ukuyaka pofuna kukuyesani.+