Aroma 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife. 2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,
18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife.
12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,