2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso naye monga mafumu.+ Tikamukana, iyenso adzatikana,+