Mateyu 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+ Luka 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano munthu wina anamufunsa kuti: “Ambuye, kodi amene akupulumuka ndi owerengeka okha?”+ Iye anawauza kuti:
14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+
23 Tsopano munthu wina anamufunsa kuti: “Ambuye, kodi amene akupulumuka ndi owerengeka okha?”+ Iye anawauza kuti: