Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+ 1 Petulo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ndipo ngati munthu wolungama adzapulumuka movutikira,+ kodi munthu wosaopa Mulungu ndi wochimwa adzaoneka n’komwe?”+
22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+
18 “Ndipo ngati munthu wolungama adzapulumuka movutikira,+ kodi munthu wosaopa Mulungu ndi wochimwa adzaoneka n’komwe?”+