Mateyu 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+ Mateyu 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ophunzirawo atamva zimenezi, anadabwa kwambiri ndipo anati: “Ndiye angapulumuke ndani?”+
14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+