Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ 3 Yohane 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe chimene chimandisangalatsa kwambiri kuposa kumva kuti ana anga akuyendabe m’choonadi.+