Agalatiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, ndine mtumwi, osati wochokera kwa anthu kapena woikidwa kudzera mwa munthu, koma kudzera mwa Yesu Khristu+ komanso kudzera mwa Mulungu Atate+ amene anamuukitsa kwa akufa.
1 Ine Paulo, ndine mtumwi, osati wochokera kwa anthu kapena woikidwa kudzera mwa munthu, koma kudzera mwa Yesu Khristu+ komanso kudzera mwa Mulungu Atate+ amene anamuukitsa kwa akufa.