Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 poika moyo wake pangozi+ pamene anakumenyerani nkhondo+ kuti akulanditseni m’manja mwa Amidiyani?+

  • 1 Samueli 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anaika moyo wake pangozi*+ n’kupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu+ kwa Aisiraeli onse. Inuyo munaona zimenezi zikuchitika, ndipo munasangalala. Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, mwa kupha Davide+ popanda chifukwa?”+

  • 1 Samueli 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno mkazi uja anapita pamene panali Sauli ndipo anaona kuti wathedwa nzeru kwambiri. Choncho anamuuza kuti: “Ineyo mtumiki wanu ndamvera mawu anu ndipo ndaika moyo wanga pangozi*+ pomvera mawu amene mwandiuza.

  • 2 Samueli 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno iye anati: “Sindingachite zimenezo+ inu Yehova! Kodi ndimwe magazi+ a amuna amene anaika miyoyo yawo pangozi kuti akatunge madziwa?” Choncho iye sanavomere kumwa madziwo.

      Izi n’zimene amuna atatu amphamvuwo anachita.

  • Yobu 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 N’chifukwa chiyani ndikuika moyo wanga pachiswe,*

      Ndiponso kuika moyo wanga m’dzanja langa?+

  • Salimo 119:109
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 109 Moyo wanga uli pangozi nthawi zonse,*+

      Koma sindinaiwale chilamulo chanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena