Genesis 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake. Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Deuteronomo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake. Machitidwe 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
23 Koma ungokhala wotsimikiza mtima kwambiri kusadya magazi,+ chifukwa magazi ndiwo moyo,+ ndipo suyenera kudya nyama pamodzi ndi moyo wake.
29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”