Levitiko 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’” Deuteronomo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+
17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’”