Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kwa nyama iliyonse yam’tchire ya padziko lapansi, ndi kwa cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, komanso kwa chokwawa chilichonse cha padziko lapansi chimene chili ndi moyo, ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya chawo.”+ Ndipo zinaterodi.

  • Levitiko 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.

  • Levitiko 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti moyo wa nyama iliyonse ndi magazi ake, chifukwa m’magazimo ndi mmene muli moyo. N’chifukwa chake ndauza ana a Isiraeli kuti: “Musamadye magazi a nyama iliyonse, chifukwa moyo wa nyama ina iliyonse ndi magazi ake.+ Aliyense wodya magaziwo ayenera kuphedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena