Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.