Salimo 119:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Zingwe za oipa zinandikulunga,+Koma ine sindinaiwale chilamulo chanu.+ Salimo 119:153 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 153 Onani kusautsika kwanga ndipo ndipulumutseni,+Pakuti sindinaiwale chilamulo chanu.+