1 Samueli 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anauza Abisai kuti: “Ayi, usamuphe. Kodi ndani anatambasula dzanja lake ndi kupha wodzozedwa wa Yehova,+ n’kukhala wopanda mlandu?”+ 2 Mbiri 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Davide kholo lake anachita.+
9 Koma Davide anauza Abisai kuti: “Ayi, usamuphe. Kodi ndani anatambasula dzanja lake ndi kupha wodzozedwa wa Yehova,+ n’kukhala wopanda mlandu?”+
2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Davide kholo lake anachita.+