Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye anati: ‘Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,

      Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.’+

  • Salimo 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+

      Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,+

      Amamupulumutsa ndi dzanja lake lamanja lamphamvu zopulumutsa.+

  • Salimo 105:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Iye anati: “Anthu inu musakhudze odzozedwa anga,+

      Ndipo aneneri anga musawachitire choipa chilichonse.”+

  • Luka 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena