Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.] Yeremiya 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+
5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]
6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+