Salimo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+ Salimo 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+ Salimo 140:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Inu Yehova, ndilanditseni kwa anthu oipa.+Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa,+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+
13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Onani mmene anthu odana nane akundisautsira,+Inu Mulungu amene mukundinyamula kundichotsa pazipata za imfa.+ Salimo 140:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 140 Inu Yehova, ndilanditseni kwa anthu oipa.+Nditetezeni kwa munthu wochita zachiwawa,+