1 Akorinto 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ndikusangalala kuti Sitefana+ ndi Fotunato ndi Akayiko ali kuno ndi ine, pakuti alowa m’malo mwanu. Filimoni 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikanakonda kumusunga kuti m’malo mwa iwe,+ apitirize kunditumikira pamene ndili m’ndende+ chifukwa cha uthenga wabwino.
17 Koma ndikusangalala kuti Sitefana+ ndi Fotunato ndi Akayiko ali kuno ndi ine, pakuti alowa m’malo mwanu.
13 Ndikanakonda kumusunga kuti m’malo mwa iwe,+ apitirize kunditumikira pamene ndili m’ndende+ chifukwa cha uthenga wabwino.