Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anaika moyo wake pangozi*+ n’kupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu+ kwa Aisiraeli onse. Inuyo munaona zimenezi zikuchitika, ndipo munasangalala. Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, mwa kupha Davide+ popanda chifukwa?”+

  • 1 Mbiri 11:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma iye anaima pakati pa mundawo n’kuulanditsa. Anapha Afilisiti moti Yehova anapereka chipulumutso+ chachikulu.+

  • Salimo 44:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndinu amene munatipulumutsa kwa adani athu,+

      Ndipo munanyazitsa anthu amene amadana nafe kwambiri.+

  • Yesaya 59:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti n’kuthandizapo, anadabwa kwambiri poona kuti palibe amene akulowererapo.+ Chotero anapulumutsa anthu ndi dzanja lake, ndipo chilungamo chake n’chimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena