Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+
17 “Kalanga ine! Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+ Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu yanu+ ndi dzanja lanu lotambasula.+ Nkhaniyi si yovuta kwa inu.+