1 Mafumu 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 (popeza adzamva za dzina lanu lalikulu,+ za dzanja lanu lamphamvu+ ndi mkono wanu wotambasuka), ndipo wabwera n’kupemphera atayang’ana nyumba ino,+ Yeremiya 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Ine ndinapanga dziko lapansi,+ anthu+ ndi nyama+ zapadziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso dzanja langa lotambasula.+ Ndipo dzikoli ndalipereka kwa amene ndikufuna.+
42 (popeza adzamva za dzina lanu lalikulu,+ za dzanja lanu lamphamvu+ ndi mkono wanu wotambasuka), ndipo wabwera n’kupemphera atayang’ana nyumba ino,+
5 ‘Ine ndinapanga dziko lapansi,+ anthu+ ndi nyama+ zapadziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso dzanja langa lotambasula.+ Ndipo dzikoli ndalipereka kwa amene ndikufuna.+