Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+

  • Salimo 115:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+

      Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+

  • Danieli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Alonda+ ndi amene alamula zimenezi. Angelo oyera* ndi amene apempha zimenezi ndi cholinga chakuti anthu adziwe kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso adziwe kuti iye akafuna kupereka ulamuliro kwa munthu aliyense, amamupatsa+ ndipo amaika ngakhale munthu wonyozeka kwambiri kuti azilamulira.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena