Salimo 89:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+ Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+