Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+

      Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+

  • Salimo 115:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu ndinu amene mwadalitsidwa ndi Yehova,+

      Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Salimo 146:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi,+

      Nyanja ndi zonse zili mmenemo.+

      Wosunga choonadi mpaka kalekale.+

  • Yesaya 44:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova, Wokuwombola+ ndiponso amene anakuumba kuyambira uli m’mimba, wanena kuti: “Ine Yehova ndachita zonse. Ndinatambasula ndekha kumwamba,+ ndi kukhazikitsa dziko lapansi.+ Kodi ndani anali nane?

  • Yesaya 45:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ineyo ndinapanga dziko lapansi+ ndipo ndinalenga munthu n’kumuikapo.+ Manja anga anatambasula kumwamba,+ ndipo nyenyezi ndi zonse zimene zili kumwambako ndimazilamulira.”+

  • Yeremiya 51:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Koma Mulungu wa Yakobo sali ngati mafanowa.+ Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Mulungu ameneyu ndiye ndodo ya cholowa chake+ ndipo dzina lake ndi Yehova wa makamu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena